2025-01-132025-01-132024Malimidwe okonzekera ndi olimba panyengo paulimi wansomba: Kugwirizanitsa ulimi wansomba ndi ulimi waziweto zing’onozing’ono. Zambia: AICCRA.https://hdl.handle.net/20.500.12348/6281Kusintha kwa nyengo ndi zina zotsatira kwabweretsa anthu ambiri obvutika pachiopsezo, kutentha kwanyengo ndi zochitika pa kusintha kwa nthawi ndi nthawi m’madera ambiri padziko lino lapansi. Kutentha koopsa, chilala, madzi osefukira komanso malimidwe amane sadziwika bwino abvutitsa alimi ndi zokolola zawo, kuopsezanso miyoyo yao. Kwa osulidwa ndi obvutika, unyinji wa anthu, ulimi wansomba ndi njira imodzi yokhazikitsara umoyo wa anthu osawerengedwa ndi anthu obvutika chifukwa chogwapo pamaziko achakudya ndi kukhala wanthanzi. Koma alimi ansomba ambiri m’Zambia apita m’mabvuto chifukwa cha nyengo yosadalirika paulimi wokhazikika wansomba.PDFCC-BY-NC-4.0csa training manualMalimidwe okonzekera ndi olimba panyengo paulimi wansomba: Kugwirizanitsa ulimi wansomba ndi ulimi waziweto zing’onozing’onoTraining Material